Leviticus 27:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka chokondwerera zaka 50, mundawo udzabwezedwa kwa munthu amene adaugulitsayo, amene mtundawo unali wake ngati choloŵa chake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka choliza lipenga mundawo ubwerere kwa iye amene adaugulitsa, kwa iye amene dzikoli ndi lakelake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa chaka chokondwerera zaka makumi asanu, mundawo udzabwezedwa kwa munthu amene anawugulitsayo, amene malowo anali ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka coliza lipenga mundawo ubwerere kwa iye amene adaugulitsa, kwa iye amene dzikoli ndi lace lace.