Leviticus 27:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwiniwake asafunse ngati nyamayo njabwino kapena njoipa, ndipo asaisinthitse. Akaisinthitsa ndi ina, imeneyo pamodzi ndi imene waisinthitsayo zidzakhala zopatulikira Chauta, ndipo sangaziwombole.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asafunse ngati yabwino kapena yoipa, kapena kuisintha; koma akaisinthatu, pamenepo iyo ndi yosinthikayo zikhale zopatulika zonse ziwiri; asamaiombola.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe amene adzaloledwa kusankha nyama yomwe ili yabwino kapena kusinthitsa. Ngati asinthitsa, nyamayo pamodzi ndi inzakeyo zidzakhala zopatulika ndipo sangaziwombole.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asafunse ngati yabwino kapena yoipa, kapena kuisintha; koma akaisinthatu, pamenepo iyo ndi yosinthikayo zikhale zopatulika zonse ziwiri; asamaiombola.