Leviticus 27:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ikakhala nyama yonga imene anthu amaperekera nsembe kwa Chauta, zonse zimene anthu amapereka kwa Chauta nzopatulika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chikakhala cha nyama imene anthu amabwera nayo ikhale chopereka cha Yehova, zonse zotere munthu akazipereka kwa Yehova zikhale zopatulika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ngati chimene anachitira lumbiro kuti apereke ndi nyama imene amapereka kukhala nsembe kwa Yehova, zonse zimene amapereka kwa Yehova nʼzopatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cikakhala ca nyama imene anthu amabwera nayo ikhale copereka ca Yehova, zonse zotere munthu akazipereka kwa Yehova zikhale zopatulika.