Leviticus 3:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono wansembe atenthe zonsezo pa guwa, kuti zikhale chakudya chotentha pa moto, chopereka kwa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wansembe azitenthe pa guwa la nsembe; ndicho chakudya cha nsembe yamoto ya kwa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wansembe awotche zonsezi pa guwa. Ichi ndi chakudya chotentha pa moto choperekedwa kwa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wansembe azitenthe pa guwa la nsembe; ndico cakudya ca nsembe yamoto ya kwa Mulungu.