Leviticus 3:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akapereka nkhosa kuti ikhale nsembe, abwere nayo pamaso pa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
akabwera nayo nkhosa kuti ikhale chopereka chake, abwere nayo pamaso pa Yehova;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati apereka nsembe ya mwana wankhosa, abwere naye pamaso pa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
akabwera nayo nkhosa kuti ikhale copereka cace, abwere nayo pamaso pa Yehova;