Leviticus 3:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pa nsembe yachiyanjanoyo yopereka kwa Chauta ndi yoyenera kuitentha pa moto, atapepo mafuta onse a nkhosayo, ndiye kuti mchira wonona wathunthu, ataudula m'tsinde pafupi ndi msana, mafuta okuta matumbo, mafuta ena onse okhala pamatumbopo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo abwere nayo nsembe yamoto ya kwa Yehova; yotengako ku nsembe yoyamika; mafuta ake, mchira wamafuta wonse, atauchotsa kufupi ku fupa la msana; naichotse mafuta akukuta matumbo, ndi mafuta onse akukhala pamatumbo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nsembe yachiyanjanopo ayenera kuchotsa ndi kubweretsa: mafuta a nkhosayo, mchira wake wonse wonona atawudulira mʼtsinde pafupi ndi fupa la msana, zamʼkati zonse ndi mafuta onse amene akuta ziwalo zamʼkatimo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo abwere nayo nsembe yamoto ya kwa Yehova; yotengako ku nsembe yoyamika; mafuta ace, mcira wamafuta wonse, ataucotsa kufupi ku pfupa lao msana; naicotse mafuta akukuta matumbo, ndi mafuta onse akukhala pamatumbo,