Leviticus 4:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo wansembeyo aviike chala chake m'magazi, ndipo pamaso pa Chauta awaze magaziwo kasanu ndi kaŵiri patsogolo pa nsalu yochinga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
naviike chala chake m'mwazi wa nsembewo, nauwaze kasanu ndi kawiri pamaso pa Yehova, chakuno cha nsalu yotchinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aviyike chala chake mʼmagaziwo ndi kuwawaza pamaso pa Yehova kasanu ndi kawiri patsogolo pa nsalu yotchinga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nabviike cala cace m'mwazi wa nsembewo, nauwaze kasanu ndi kawiri pamaso pa Yehova, cakuno ca nsaru yocinga.