Leviticus 4:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uza Aisraele kuti pa zonse zimene Chauta adaletsa, munthu aliyense akachimwapo mosadziŵa, pochita kanthu kena kalikonse koletsedwa, azichita izi:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lankhula ndi ana a Israele, ndi kuti, Munthu akachimwa, osati dala, pa china cha zinthu zilizonse aziletsa Yehova, nakachitapo kanthu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Awuze Aisraeli kuti, ‘Munthu akachimwa mosadziwa ndi kuchita chilichonse chimene Yehova walamula kuti asachite, azichita izi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lankhula ndi ana a Israyeli, ndi kuti, Munthu akacimwa, osati dala, pa cina ca zinthu ziri zonse aziletsa Mulungu, nakacitapo kanthu;