Leviticus 4:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Wolamula akachimwa mosadziŵa, kuchimwira Chauta, Mulungu wake, pa chinthu choletsedwa, napalamula pakutero,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akachimwa mkulu, osati dala, pa china cha zinthu zilizonse aziletsa Yehova Mulungu wake, napalamula;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ngati mtsogoleri achimwa mosadziwa nachita zimene ndi zoletsedwa ndi Yehova Mulungu wake, ndiye kuti wapalamula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akacimwa mkuru, osati dala, pa cina ca zinthu ziti zonse aziletsa Yehova Mulungu wace, naparamula;