Leviticus 4:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pambuyo pake ena nkumudziŵitsa za tchimo lakelo, iyeyo apereke nsembe ya tonde wopanda chilema.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
akamdziwitsa kuchimwa kwake adachimwako, azidza nacho chopereka chake, ndicho tonde wopanda chilema;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ngati wauzidwa za tchimo limene wachita, iye abwere ndi mbuzi yayimuna yopanda chilema kuti ikhale chopereka chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
akamdziwitsa kucimwa kwace adacimwako, azidza naco copereka cace, ndico tonde wopanda cirema;