Leviticus 4:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atatero, wansembe atengeko magazi ndi chala chake, ndi kuŵapaka pa nyanga za guwa la nsembe zopsereza, ndipo magazi otsalawo aŵathire patsinde pa guwa lomwelo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wansembe atengeko mwazi ndi chala chake, nauike pa nyanga za guwa la nsembe yopsereza, ndi kuthira mwazi wake wonse patsinde pa guwa la nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo wansembe atenge magazi ndi chala chake ndi kuwapaka pa nyanga za guwa lansembe zopsereza ndi kuthira magazi wotsalawo pa tsinde la guwalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wansembe atengeko mwazi ndi cala cace, nauike pa nyanga za guwa la nsembe yopsereza, ndi kuthira mwazi wace wonse patsinde pa guwa la nsembe.