Leviticus 4:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo asanjike dzanja lake pamutu pa nkhosa ya nsembe yopepesera machimoyo, ndi kuiphera pa malo amene amaphera nsembe yopsereza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Naike dzanja lake pa mutu wa nsembe yauchimo, ndi kuipha ikhale nsembe yauchimo pamalo pophera nsembe yopsereza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asanjike dzanja lake pa mutu wa mwana wankhosayo ndipo amuphe pamalo pamene amaphera chopereka chopsereza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Naike dzanja lace pa mutu wa nsembe yaucimo, ndi kuipha ikhale nsembe yaucimo pamalo pophera nsembe yopsereza.