Leviticus 6:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kapena kunama kuti sadatole zimene zidatayika, kapena kumalumbira zonama pa kanthu kalikonse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kapena anapeza chinthu chotayika, nanenapo bodza, nalumbira pabodza; pa chimodzi cha izi zonse amachita munthu, ndi kuchimwapo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kapena ndi kunama kuti sanatole chinthu chimene chinatayika, kapena kulumbira mwachinyengo pa chinthu chilichonse chimene munthu akachita amachimwa nacho,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kapena anapeza cinthu cotayika, nanenapo bodza, nalumbira pabodza; pa cimodzi ca izi zonse amacita munthu, ndi kucimwapo;