Leviticus 7:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uza Aisraele kuti asadye mafuta ang'ombe, kapena ankhosa kapenanso ambuzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lankhula ndi ana a Israele ndi kuti, Musamadya mafuta ali onse, a ng'ombe, kapena a nkhosa, kapena a mbuzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Awuze Aisraeli kuti, ‘Musadye mafuta a ngʼombe, nkhosa kapenanso mbuzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lankhula ndi ana a Israyeli ndi kuti, Musamadya mafuta ali onse, a ng'ombe, kapena a nkhosa, kapena a mbuzi.