Leviticus 7:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiponso kulikonse kumene akakhale, asadye magazi aliwonse, ambalame kapena anyama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo musamadya mwazi uliwonse, kapena wa mbalame, kapena wa nyama, m'nyumba zanu zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo kulikonse kumene mukakhale musakadye magazi a mbalame iliyonse kapena magazi a nyama iliyonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo musamadya mwazi uti wonse, kapena wa mbalame, kapena wa nyama, m'nyumba zanu zonse,