Leviticus 7:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uza Aisraele kuti, ‘Munthu amene apereka nsembe yake yachiyanjano kwa Chauta, abwere ndi gawo la nsembeyo kwa Chauta. Pa nsembe yake yachiyanjanoyo
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lankhula ndi ana a Israele, ndi kuti, Wakubwera nayo nsembe yoyamika yake kwa Yehova, azidza nacho chopereka chake kwa Yehova chochokera ku nsembe yoyamika yake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Awuze Aisraeli kuti, Aliyense amene apereka nsembe yachiyanjano kwa Yehova, abwere ndi gawo la nsembeyo kwa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lankhula ndi ana a Israyeli, ndi kuti, Wakubwera nayo nsembe yoyamika yace kwa Yehova, azidza naco copereka cace kwa Yehova cocokera ku nsembe yoyamika yace;