Leviticus 7:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wansembe mumpatsenso ntchafu ya ku dzanja lamanja, kuti ikhale chopereka cha pa nsembe yanu yachiyanjano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwendo wathako wa ku dzanja lamanja muupereke kwa wansembe ukhale nsembe yokweza yochokera ku nsembe zoyamika zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumupatse wansembe ntchafu ya kumanja ya nsembe yanu yachiyanjano kuti ikhale chopereka chanu kwa iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwendo wathako wa ku dzanja lamanja muupereke kwa wansembe, ukhale nsembe yokweza yocokera ku nsembe zoyamika zanu.