Leviticus 7:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakati pa ana a Aroni, wansembe amene apereka magazi ndi mafuta a nsembe yachiyanjano, ndiye adzalandire ntchafu ya ku dzanja lamanja ngati chigawo chake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwendo wathako wa ku dzanja lamanja ukhale gawo lake la iyeyu mwa ana a Aroni wakubwera nao mwazi wa zopereka zoyamika, ndi mafuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wa Aaroni amene amapereka magazi ndi mafuta a nsembe yachiyanjano, adzitenga ntchafu ya kumanja kukhala gawo lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwendo wathako wa ku dzanja lamanja ukhale gawo lace la iyeyu mwa ana a Aroni wakubwera Ilao mwazi wa zopereka zoyamika, ndi mafuta.