Leviticus 8:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
adazikhazika m'manja mwa Aroni ndi m'manja mwa ana ake, ndipo adaziweyula kuti zikhale zopereka zoweyula kwa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
anaika zonsezi m'manja mwa Aroni, ndi m'manja mwa ana ake amuna, naziweyula nsembe yoweyula pamaso pa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anapereka zonsezi mʼmanja mwa Aaroni ndi ana ake amene anazipereka kwa Yehova kuti zikhale nsembe yoweyula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
anaika zonsezi m'manja mwa Aroni, ndi m'manja mwa ana ace amuna, naziweyula nsembe yoweyula pamaso pa Yehova.