Leviticus 8:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adatilamula kuti tikuchiteni zimene takuchitanizi, kuti ukhale mwambo wopepesera machimo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga anachita lero lino, momwemo Yehova anauza kuchita, kukuchitirani chotetezera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimene zachitika lerozi analamula ndi Yehova kuti zichitike ngati nsembe yopepesera machimo anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga anacita lero lino, momwemo Yehova anauza kucita, kukucitirani cotetezera.