Leviticus 9:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mafuta ndi imso, pamodzi ndi mphumphu ya mafuta akuchiŵindi, za nsembe yopepesera machimoyo, adazitenthera pa guwa, monga momwe Chauta adaalamulira Mose.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma mafutawo, ndi impso, ndi chokuta cha mphafa za nsembe yauchimo, anazitentha pa guwa la nsembe; monga Yehova anauza Mose.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anatentha paguwapo, mafuta, impsyo pamodzi ndi mafuta amene amakuta chiwindi ngati nsembe yopepesera machimoyo, monga momwe Yehova analamulira Mose.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma mafutawo, ndi imso, ndi cokuta ca mphafa za nsembe yaucimo, anazitentha pa guwa la nsembe; monga Yehova anauza Mose.