Leviticus 9:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyama yake ndi chikopa chake, adazitenthera kunja kwake kwa mahema.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatentha ndi moto nyamayi ndi chikopa kunja kwa chigono.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma nyama ndi chikopa anazitenthera kunja kwa msasa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatentha ndi moto nyamayi ndi cikopa kunja kwa cigono.