Leviticus 9:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaperekanso chopereka cha chakudya, natapako ufawo dzanja limodzi nautentha pa guwa, kuwonjezera pa nsembe yopsereza yam'maŵayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anabwera nayo nsembe yaufa, natengako wodzala dzanja, nautentha pa guwa la nsembe, angakhale adatentha nsembe yopsereza ya m'mawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anabweranso ndi chopereka cha chakudya. Anatapa ufa dzanja limodzi ndi kutentha pa guwa, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya mmawa ija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anabwera nayo nsembe yaufa, natengako wodzala dzanja, nautentha pa guwa la nsembe, angakhale adatentha nsembe yopsereza ya m'mawa.