Leviticus 9:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adampatsiranso mafuta ang'ombe ndi mafuta a nkhosa yamphongo, mchira wamafuta, mafuta okuta matumbo, imso pamodzi ndi mphumphu ya mafuta akuchiŵindi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mafuta a ng'ombe; ndi a nkhosa yamphongoyo, ndi mchira wamafuta, ndi chophimba matumbo, ndi impso, ndi chokuta cha mphafa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anamupatsiranso mafuta a ngʼombeyo ndi nkhosa yayimunayo: mchira wamafuta, mafuta wokuta matumbo, impsyo ndi mafuta wokuta chiwindi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi a nkhosa, ndi mcira wamafuta, ndi cophimba matumbo, ndi imso, ndi cokuta ca mphafa;