Leviticus 9:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anawo adaika mafuta pa nganga, ndipo Aroni adatentha mafutawo pa guwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anaika mafuta pa ngangazo, natentha mafutawo pa guwa la nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Aaroni anayika mafutawo pa zidale. Pambuyo pake Aaroni anatentha mafutawo pa guwa lansembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anaika mafuta pa ngangazo, natentha mafutawo pa guwa la nsembe.