Leviticus 9:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Aroni adaweyula ngangazo ndi ntchafu ya ku dzanja lamanja, kuti zikhale chopereka choweyula pamaso pa Chauta, monga momwe Mose adaalamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Aroni anaweyula ngangazo ndi mwendo wathako wa ku dzanja lamanja zikhale nsembe yoweyula pamaso pa Yehova; monga Iye anauza Mose.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma zidale ndi ntchafu ya kumanja Aaroni anaziweyula ngati chopereka choweyula pamaso pa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Aroni anaweyula ngangazo ndi mwendo wathako wa ku dzanja lamanja zikhale nsembe yoweyula pamaso pa Yehova; monga iye anauza Mose.