Leviticus 9:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Aroni adasendera pafupi ndi guwa, napha mwanawang'ombe woperekera nsembe yopepesera machimo, nsembeyo ya iye mwini wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Aroni anasendera kufupi kwa guwa la nsembe, napha mwanawang'ombe wa nsembe yauchimo, ndiyo ya kwa iye yekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Aaroni anasendera pafupi ndi guwa, napha mwana wangʼombe uja kukhala nsembe yake yopepesera machimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Aroni anasendera kufupi kwa guwa la nsembe, napha mwana wa ng'ombe wa nsembe yaucimo, ndiyo ya kwa iye yekha.