Luke 1:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi yonseyo anthu aja ankadikira Zakariya, nkumadabwa kuti akuchedwa m'Nyumba ya Mulungumo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu analikulindira Zekariya, nazizwa ndi kuchedwa kwake m'Kachisimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawiyi, anthu ankadikira Zakariya ndipo anadabwa chifukwa anatenga nthawi yayitali ali mʼNyumba ya Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu analikulindira Zakariya, nazizwa ndi kucedwa kwace m'kacisimo.