Luke 1:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atatha masiku ake otumikira m'Nyumba ya Mulungu, adapita kwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, pamene masiku a utumiki wake anamalizidwa, anamuka kunyumba kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi yake yotumikira itatha, anabwerera kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, pamene masiku a utumiki wace anamarizidwa, anamuka kunyumba kwace.