Luke 1:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake mkazi wake Elizabeti adatenga pathupi, nabindikira miyezi isanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atatha masiku awa, Elizabeti mkazi wake anaima; nadzibisa miyezi isanu, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zitatha izi, mkazi wake Elizabeti anakhala ndi pakati ndipo anadzibisa kwa miyezi isanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atatha masiku awa, Elisabeti mkazi wace anaima; nadzibisa miyezi isanu, nati,