Luke 1:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maria adadzidzimuka nawo kwambiri mau ameneŵa, nayamba kusinkhasinkha kuti kodi moni umenewu ndi wa mtundu wanji?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iye ananthunthumira ndi mau awa, nasinkhasinkha kulonjera uku nkutani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mariya anavutika kwambiri ndi mawu awa ndipo anadabwa ndi kulonjera kotere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye ananthunthumira ndi mau awa, nasinkhasinkha kulankhula uku nkutani.