Luke 1:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita masiku oŵerengeka, Maria adanyamuka napita mofulumira ku dera lamapiri, ku mudzi wina wa ku Yudeya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Maria ananyamuka masiku amenewa, namuka ndi changu kudziko la mapiri kumudzi wa Yuda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi imeneyo anakonzeka ndipo anapita mofulumira ku mudzi wa ku mapiri a dziko la Yudeya,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mariya ananyamuka masiku amenewa, namuka ndi cangu ku dziko la mapiri ku mudzi wa Yuda;