Luke 1:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adakaloŵa m'nyumba ya Zakariya, malonjera Elizabeti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nalowa m'nyumba ya Zekariya, nalonjera Elizabeti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kumene anakalowa mʼnyumba ya Zakariya nalonjera Elizabeti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nalowa m'nyumba ya Zakariya, nalankhula Elisabeti.