Luke 1:43 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndine yani kuti inu, mai wa Ambuye anga, mudzandiyendere?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ichi chichokera kuti kudza kwa ine, kuti adze kwa ine amake wa Ambuye wanga?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma nʼchifukwa chiyani andikomera mtima kuti amayi a Ambuye anga abwere kwa ine?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ici cicokera kuti kudza kwa ine, kuti adze kwa ine amace wa Ambuye wanga?