Luke 1:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
popeza kuti wayang'ana kutsika kwa mtumiki wake. Ndithu kuyambira tsopano anthu a mibadwo yonse adzanditcha wodala,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa Iye anayang'anira umphawi wa mdzakazi wake; pakuti taonani, kuyambira tsopano, anthu a mibadwo yonse adzanditchula ine wodala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti wakumbukira kudzichepetsa kwa mtumiki wake. Kuyambira tsopano mibado yonse idzanditcha wodala,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa iye anayang'anira umphawi wa mdzakazi wace; Pakuti taonani, kuyambira tsopano, anthu a mibadwo yonse adzandichula ine wodala.