Luke 1:49 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti Iye amene ali wamphamvu wandichitira zazikulu, ndipo dzina lake nloyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa Iye Wamphamvuyo anandichitira ine zazikulu; ndipo dzina lake lili loyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti Wamkuluyo wandichitira ine zinthu zazikulu, dzina lake ndi loyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa iye Wamphamvuyo anandicitira ine zazikuru; 4 Ndipo dzina lace liri loyera.