Luke 1:52 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafumu amphamvu waŵatsitsa pa mipando yao yachifumu, anthu wamba nkuŵakweza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye anatsitsa mafumu pa mipando yao yachifumu, ndipo anakweza aumphawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anachotsa olamulira pa mipando yawo yaufumu, koma wakweza odzichepetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iye anatsitsa mafumu pa mipando yao yacifumu, Ndipo anakweza aumphawi,