Luke 1:53 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu anjala waŵakhutitsa ndi zabwino, anthu olemera nkuŵabweza osaŵapatsa kanthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anawakhutitsa anjala ndi zinthu zabwino, ndipo eni chuma anawachotsa opanda kanthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye wakhutitsa a njala ndi zinthu zabwino koma anachotsa olemera wopanda kanthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
7 Anawakhutitsa anjala ndi zinthu zabwino, Ndipo eni cuma anawacotsa opanda kanthu.