Luke 1:55 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Izi ndi zomwe adaalonjeza kuti adzaŵachitira makolo athu akale aja, Abrahamu ndi zidzukulu zake mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
(Monga analankhula kwa makolo athu) kwa Abrahamu ndi kwa mbeu yake kunthawi yonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa Abrahamu ndi zidzukulu zake ku nthawi zonse monga ananena kwa makolo athu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
8 (Monga analankhula kwa makolo athu) Kwa Abrahamu ndi kwa mbeu yace ku nthawi yonse.