Luke 1:57 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi yakuti Elizabeti achire idakwana, ndipo adabala mwana wamwamuna.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo inakwanira nthawi ya Elizabeti, ya kubala kwake, ndipo anabala mwana wamwamuna.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Itakwana nthawi yoti Elizabeti abereke, anabereka mwana wamwamuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo inakwanira nthawi ya Elisabeti, ya kubala kwace, ndipo anabala mwana wamwamuna.