Luke 1:61 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo anthuwo adamuuza kuti, “Koma pakati pa abale anu palibe amene ali ndi dzina limeneli.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo anati kwa iye, Palibe wina wa abale ako amene atchedwa dzina ili.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anati kwa iye, “Palibe mmodzi mwa abale ake amene ali ndi dzina limeneli.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo anati kwa iye, Palibe wina wa abale ako amene achedwa dzina ili.