Luke 1:68 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Atamandike Ambuye, Mulungu wa Aisraele, chifukwa adadzayendera anthu ao, ndi kudzaŵaombola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wolemekezeka Ambuye, Mulungu wa Israele; chifukwa Iye anayang'ana, nachitira anthu ake chiombolo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Alemekezeke Ambuye, Mulungu wa Israeli chifukwa wabwera ndi kuwombola anthu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolemekezeka Ambuye, Mulungu wa Israyeli; 14 Cifukwa iye anayang'ana, nacitira anthu ace ciombolo,