Luke 1:69 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adautsa wina, wa fuko la mtumiki wake Davide, kuti akhale Mpulumutsi wathu wamphamvu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anatikwezera ife nyanga ya chipulumutso, mwa fuko la Davide mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye wakweza nyanga yachipulumutso kwa ife mu nyumba ya mtumiki wake Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anatikwezera ife nyanga ya cipulumutso, Mwa pfuko la Davine mwana wace,