Luke 1:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaalibe mwana, chifukwa Elizabeti anali wosabala, ndipo aŵiri onsewo anali okalamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analibe mwana, popeza Elizabeti anali wouma, ndipo onse awiri anakalamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma analibe ana chifukwa Elizabeti anali wosabereka; ndipo onse anali okalamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analibe mwana, popeza Elisabeti anali wouma, ndipo onse awiri anakalamba.