Luke 1:71 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaalonjeza kuti adzatipulumutsa kwa adani athu, ndi kwa onse odana nafe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chipulumutso cha adani athu, ndi pa dzanja la anthu onse amene atida ife.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chipulumutso kuchoka kwa adani athu ndi kuchoka mʼdzanja la onse otida,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cipulumutso ca adani athu, ndi pa dzanja la anthu onse amene atida ife;