Luke 1:75 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti tikhale oyera mtima ndi olungama pamaso pake, masiku onse a moyo wathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
m'chiyero ndi chilungamo pamaso pake, masiku athu onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mʼchiyero ndi mʼchilungamo masiku athu onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
18 M'ciyero ndi cilungamo pamaso pace, masiku athu onse.