Luke 1:76 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mwana iwe, udzatchedwa mneneri wa Mulungu Wopambanazonse, chifukwa udzatsogola pamaso pa Ambuye, kuti ukonzeretu njira zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Eya, ndipo iwetu kamwanawe, udzanenedwa mneneri wa Wamkulukulu; pakuti udzatsogolera Ambuye, kukonza njira zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndipo iwe mwana wanga udzatchedwa mneneri wa Wammwambamwamba; pakuti udzapita patsogolo pa Ambuye kukonza njira yake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
19 Eya, ndipo iwetu kamwanawe, udzanenedwa mneneri wa Wamkulukulu: 20 Pakuti udzatsogolera Ambuye, kukonza njira zace;