Luke 1:77 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udzadziŵitsa anthu ao kuti Mulungu adzaŵapulumutsa pakuŵakhululukira machimo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuwapatsa anthu ake adziwitse chipulumutso, ndi makhululukidwe a machimo ao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kupatsa anthu ake chidziwitso cha chipulumutso kudzera mwa chikhululukiro cha machimo awo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuwapatsa anthu ace adziwitse cipulumutso, 21 Ndi makhululukidwe a macimoao,