Luke 10:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndiye zidangochitika kuti wansembe wina ankapita pa njira yomweyo. Pamene adaona munthu uja, adangolambalala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudangotero kuti wansembe wina anatsika njirayo, ndipo pakumuona iye anapita mbali ina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wansembe ankapita pa njira yomweyo, ndipo ataona munthuyo, analambalala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudangotero kuti wansembe wina anatsika njirayo, ndipo pakumuona iye anapita mbali yina.