Luke 10:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musatenge chikwama cha ndalama, kapena thumba lapaulendo, kapenanso nsapato zapadera ai. Musaimenso kuti mupereke moni pa njira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musanyamule thumba la ndalama kapena thumba la kamba, kapena nsapato; nimusalonjere munthu panjira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musatenge chikwama kapena thumba kapena nsapato; ndipo musalonjere wina aliyense pa njira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musanyamule thumba la ndalama kapena thumba la kamba, kapena nsapato; nimusalankhule munthu panjira.